Uwu Ndi Moyo Wanga Watsopano ndi bukhu loyamba mwa mabukhu anayi a mndandandawa Foundations for Living Discipleship Series. M'bukhuli anthu amafunsidwa ndi kuyambitsidwa kudziwa Yesu Khristu ndipo alimbikitsidwa kukhala ophunzira ake. Komabe, ophunzira adzazindikira posachedwa kuti phunziroli silili kwa amene akuphunzira za kukhala ophunzira koyamba kokha. Ophunzira akuluakulu a Yesu adzapindula akabwerezanso njira wmwe adadutsa kuti akhale ophunzira ndipo adzakula mwauzimu pogwiritsa ntchito mfundo zokhudzana ndi kukhala ophunzira.